Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 22:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zochita zake zonse, komanso nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga, ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.

  • Salimo 45:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+

      Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+

  • Amosi 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anthu inu mukugona pamipando ya minyanga ya njovu+ ndi kudziwongola pamabedi, ndiponso mukudya nyama ya ana a nkhosa ndi ana amphongo onenepa a ng’ombe zanu.+

  • Chivumbulutso 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 katundu yense+ wagolide, siliva, mwala wamtengo wapatali, ndi ngale. Komanso palibe wowagula nsalu zabwino kwambiri, zofiirira, zasilika, zofiira kwambiri, ndi mtengo uliwonse wa fungo lokoma, komanso chilichonse chopangidwa ndi mnyanga, chilichonse chopangidwa ndi mtengo wapamwamba, ndi chamkuwa, chachitsulo, ndi chamwala wa mabo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena