1 Mafumu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide,+ siliva, minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko. Ezekieli 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Dedani+ unali kuchita nawo malonda, ndipo unalemba ntchito zilumba zambiri kuti zizikuchitira malonda. Anthu a m’zilumbazo anali kukulipira minyanga+ komanso mitengo ya phingo.
22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide,+ siliva, minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.
15 Ana a Dedani+ unali kuchita nawo malonda, ndipo unalemba ntchito zilumba zambiri kuti zizikuchitira malonda. Anthu a m’zilumbazo anali kukulipira minyanga+ komanso mitengo ya phingo.