Genesis 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Kusi anali Seba,+ Havila, Sabita, Raama+ ndi Sabiteka. Ana a Raama anali Sheba ndi Dedani.+ 1 Mbiri 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana a Kusi anali Seba,+ Havila, Sabita,+ Raama,+ ndi Sabiteka.+ Ana a Raama anali Sheba ndi Dedani.+ Yeremiya 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndinamwetsanso Dedani,+ Tema,+ Buza, onse odulira ndevu zawo zam’mbali,+
9 Ana a Kusi anali Seba,+ Havila, Sabita,+ Raama,+ ndi Sabiteka.+ Ana a Raama anali Sheba ndi Dedani.+