Ezekieli 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Unali kuchita malonda ndi amalonda a ku Sheba+ ndi ku Raama.+ Unali kuwapatsa zinthu zako zimene unasunga, posinthanitsa ndi mtundu ulionse wa mafuta onunkhira abwino kwambiri, mtundu uliwonse wa miyala yamtengo wapatali ndi golide.+
22 Unali kuchita malonda ndi amalonda a ku Sheba+ ndi ku Raama.+ Unali kuwapatsa zinthu zako zimene unasunga, posinthanitsa ndi mtundu ulionse wa mafuta onunkhira abwino kwambiri, mtundu uliwonse wa miyala yamtengo wapatali ndi golide.+