1 Mafumu 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila+ zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo n’kuyamba kunena zonse zimene zinali kumtima kwake.+ Yesaya 60:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chikhamu cha ngamila zamphongo zing’onozing’ono za ku Midiyani ndi ku Efa+ chidzadzaza dziko lako. Anthu onse a ku Sheba+ adzabwera atanyamula golide ndi lubani. Iwo adzatamanda Yehova pamaso pa anthu onse.+
2 Mfumukaziyo inafika ku Yerusalemu ndi anthu ambiri oiperekeza.+ Inabwera ndi ngamila+ zitanyamula mafuta a basamu,+ golide wambiri, ndi miyala yamtengo wapatali. Inafika kwa Solomo n’kuyamba kunena zonse zimene zinali kumtima kwake.+
6 Chikhamu cha ngamila zamphongo zing’onozing’ono za ku Midiyani ndi ku Efa+ chidzadzaza dziko lako. Anthu onse a ku Sheba+ adzabwera atanyamula golide ndi lubani. Iwo adzatamanda Yehova pamaso pa anthu onse.+