1 Mbiri 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ana a Midiyani anali Efa,+ Eferi, Hanoki, Abida, ndi Elida.+ Onsewa anali ana aamuna a Ketura.