Nyimbo ya Solomo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mafuta+ ako odzola ndi onunkhira bwino. Dzina lako lili ngati mafuta othira pamutu.+ N’chifukwa chake atsikana amakukonda. Nyimbo ya Solomo 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 maluwa a safironi,+ mabango onunkhira,+ sinamoni,+ komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+ ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+
3 Mafuta+ ako odzola ndi onunkhira bwino. Dzina lako lili ngati mafuta othira pamutu.+ N’chifukwa chake atsikana amakukonda.
14 maluwa a safironi,+ mabango onunkhira,+ sinamoni,+ komanso mitengo yosiyanasiyana ya lubani, mule, aloye,+ ndi zonunkhira zonse zabwino kwambiri.+