Ekisodo 30:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana. Ezekieli 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Unali kuchita malonda ndi amalonda a ku Sheba+ ndi ku Raama.+ Unali kuwapatsa zinthu zako zimene unasunga, posinthanitsa ndi mtundu ulionse wa mafuta onunkhira abwino kwambiri, mtundu uliwonse wa miyala yamtengo wapatali ndi golide.+ 2 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma tiyamike Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera+ pamodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadirira kupambana.+ Kudziwa Mulungu kuli ngati fungo lonunkhira bwino ndipo kudzera mu ntchito yathu fungoli likufalikira paliponse.+
34 Ndiyeno Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Tenga zonunkhira izi:+ madontho a sitakate,* onika, mafuta onunkhira a galibanamu ndi lubani*+ weniweni. Zonsezi zikhale za muyezo wofanana.
22 Unali kuchita malonda ndi amalonda a ku Sheba+ ndi ku Raama.+ Unali kuwapatsa zinthu zako zimene unasunga, posinthanitsa ndi mtundu ulionse wa mafuta onunkhira abwino kwambiri, mtundu uliwonse wa miyala yamtengo wapatali ndi golide.+
14 Koma tiyamike Mulungu amene nthawi zonse amatitsogolera+ pamodzi ndi Khristu ngati kuti tikuguba pa chionetsero chonyadirira kupambana.+ Kudziwa Mulungu kuli ngati fungo lonunkhira bwino ndipo kudzera mu ntchito yathu fungoli likufalikira paliponse.+