Ekisodo 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250. Yesaya 43:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira+ ndi ndalama iliyonse, ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Koma m’malomwake, wandiumiriza ndi machimo ako kuti ndikutumikire. Wanditopetsa ndi zolakwa zako.+
23 “Koma iweyo utenge mafuta awa onunkhira, abwino koposa:+ madontho oundana a mule*+ masekeli 500, sinamoni*+ wonunkhira bwino hafu ya muyezo wa mule, kapena kuti masekeli 250, ndi kalamasi* wonunkhira+ wokwana masekeli 250.
24 Iwe sunandigulire bango lonunkhira+ ndi ndalama iliyonse, ndipo sunandikhutitse ndi mafuta a nsembe zako.+ Koma m’malomwake, wandiumiriza ndi machimo ako kuti ndikutumikire. Wanditopetsa ndi zolakwa zako.+