Ezekieli 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Vedani ndi Yavani akudera la Uzali anakupatsa katundu wawo kuti iwe uwapatse katundu amene unasunga. Iwo anakupatsa ziwiya zachitsulo, mitengo ya kasiya ndi mabango onunkhira+ posinthanitsa ndi katundu wako.
19 Vedani ndi Yavani akudera la Uzali anakupatsa katundu wawo kuti iwe uwapatse katundu amene unasunga. Iwo anakupatsa ziwiya zachitsulo, mitengo ya kasiya ndi mabango onunkhira+ posinthanitsa ndi katundu wako.