Numeri 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda m’mphepete mwa mtsinje.+Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anabzala,Ngati mikungudza m’mbali mwa madzi.+ Salimo 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+
6 Andanda kukafika kutali ngati zigwa,*+Ngati minda m’mphepete mwa mtsinje.+Ngati mitengo ya aloye imene Yehova anabzala,Ngati mikungudza m’mbali mwa madzi.+
8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+