Salimo 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zako zonse ndi zothiridwa mafuta onunkhira a mule, aloye ndi kasiya.*Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera mʼchinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:8 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 92/1/2014, tsa. 10 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2139
8 Zovala zako zonse ndi zothiridwa mafuta onunkhira a mule, aloye ndi kasiya.*Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera mʼchinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.