Salimo 45:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 45:8 Nsanja ya Olonda,2/15/2014, tsa. 92/1/2014, tsa. 10 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2139
8 Zovala zako zonse ndi zonunkhira mafuta a mule, aloye ndi kasiya.*+Umasangalala ndi nyimbo zoimbidwa ndi zipangizo za zingwe, kuchokera m’chinyumba chachikulu cha mfumu, chokongoletsedwa ndi minyanga ya njovu.+