-
Nyimbo ya Solomo 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ine ndinadzuka kuti ndimutsegulire wachikondi wanga ndipo manja anga anali kuyenderera mafuta a mule. Zala zanga zinali kuyenderera mule pamene ndinali kugwira pabowo lolowetsapo loko wa pachitseko.
-