1 Samueli 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+ Miyambo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+ Miyambo 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawu okoma ali ngati chisa cha uchi.+ Amakhala okoma kwa munthu ndipo amachiritsa mafupa.+ Machitidwe 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Abale akumeneko atamva za ife, anabwera kudzatichingamira ku Msika wa Apiyo ndi ku Nyumba Zitatu za Alendo. Paulo atawaona, anayamika Mulungu, ndipo analimba mtima.+
16 Tsopano Yonatani mwana wa Sauli ananyamuka ndi kupita kwa Davide ku Horesi, kuti akalimbikitse+ Davide kudalira Mulungu.+
23 Munthu amasangalala ndi yankho lochokera pakamwa pake,+ ndipo mawu onenedwa pa nthawi yoyenera ndi abwino kwambiri.+
15 Abale akumeneko atamva za ife, anabwera kudzatichingamira ku Msika wa Apiyo ndi ku Nyumba Zitatu za Alendo. Paulo atawaona, anayamika Mulungu, ndipo analimba mtima.+