Ezekieli 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘“Tarisi+ unali kuchita naye malonda a zinthu zambiri zosiyanasiyana zamtengo wapatali.+ Unamupatsa zinthu zako zimene unasunga posinthanitsa ndi siliva, chitsulo, tini ndi mtovu.+
12 “‘“Tarisi+ unali kuchita naye malonda a zinthu zambiri zosiyanasiyana zamtengo wapatali.+ Unamupatsa zinthu zako zimene unasunga posinthanitsa ndi siliva, chitsulo, tini ndi mtovu.+