2 Mbiri 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+ 2 Mbiri 20:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Chotero anayamba kugwira naye limodzi ntchito yopanga zombo zopita ku Tarisi.+ Zombozo anazipangira ku Ezioni-geberi.+ Salimo 72:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+
21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+
36 Chotero anayamba kugwira naye limodzi ntchito yopanga zombo zopita ku Tarisi.+ Zombozo anazipangira ku Ezioni-geberi.+
10 Mafumu a ku Tarisi ndi m’zilumba+Adzapereka msonkho.+Mafumu a ku Sheba ndi SebaAdzapereka mphatso.+