Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+

  • 1 Mafumu 10:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide,+ siliva, minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.

  • Yesaya 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Lidzafikira zombo zonse za ku Tarisi,+ ndi ngalawa zonse zabwinozabwino.

  • Yona 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo Yona ananyamuka n’kulowera ku Tarisi,+ kuthawa Yehova.+ Kenako anafika ku Yopa+ ndipo kumeneko anapeza chombo chopita ku Tarisi. Iye analipira malipiro a ulendowo n’kukwera chombocho kuti apite ku Tarisi limodzi ndi anthu amene anali m’chombomo, kuthawa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena