Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+

  • 2 Mbiri 9:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 pakuti zombo za mfumu zinkapita ku Tarisi+ limodzi ndi atumiki a Hiramu.+ Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombo za ku Tarisizo zinkabweretsa golide, siliva,+ minyanga ya njovu,+ anyani, ndi mbalame zotchedwa pikoko.+

  • Yesaya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+

  • Yeremiya 10:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Siliva wosulidwa kukhala mapalemapale amachokera ku Tarisi+ ndipo golide amachokera ku Ufazi.+ Zonsezi zimakonzedwa mwaluso, ndipo ndi ntchito ya manja a mmisiri wa zitsulo. Mafanowo amawaveka zovala zaulusi wabuluu ndi ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira. Nawonso angokhala ntchito ya amisiri aluso.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena