Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 mafumu onse a Turo,+ mafumu onse a Sidoni+ ndi mafumu a pachilumba cha m’nyanja.

  • Yeremiya 47:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Iwo adzachita mantha chifukwa cha tsiku limene likubwera. Tsikuli ndi lofunkha zinthu za Afilisiti+ onse ndi kupha wopulumuka aliyense wothandiza+ Turo+ ndi Sidoni.+ Pakuti Yehova adzafunkha zinthu za Afilisiti+ amene atsala ochokera pachilumba cha Kafitori.+

  • Ezekieli 26:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa chifukwa chimenechi, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ine ndikuukira iwe Turo ndipo ndikutumizira mitundu yambiri ya anthu+ kuti idzamenyane nawe. Anthuwo adzabwera ngati mafunde a m’nyanja.+

  • Ezekieli 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, imba nyimbo yoimba polira+ yokhudza Turo.

  • Yoweli 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Tsopano ndili nawenso chiyani iwe Turo ndi Sidoni+ ndiponso inu nonse okhala m’chigawo cha Filisitiya?+ Kodi zimenezi ndi zimene mukundipatsa monga mphoto yanga? Ngati mukundipatsa zimenezi, ine ndidzakubwezerani mwamsanga ndiponso mofulumira zimene mwandichitirazo.+

  • Amosi 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Yehova wanena kuti, ‘Popeza kuti Turo+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo, ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pa ubale.+

  • Zekariya 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova adzamulanda chuma chake ndipo gulu lake lankhondo adzaliphera m’nyanja.+ Koma iye adzatenthedwa ndi moto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena