1 Mafumu 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zochita zake zonse, komanso nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga, ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zochita zake zonse, komanso nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga, ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.