1 Mafumu 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhani zina zokhudza Basa ndi zimene anachita ndiponso zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Nkhani zina zokhudza Omuri, zimene anachita ndi zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
5 Nkhani zina zokhudza Basa ndi zimene anachita ndiponso zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
27 Nkhani zina zokhudza Omuri, zimene anachita ndi zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.