1 Mafumu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhani zina zokhudza Basa ndi zimene anachita ndiponso zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu 22:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zochita zake zonse, komanso nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga, ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
5 Nkhani zina zokhudza Basa ndi zimene anachita ndiponso zochita zake zamphamvu, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
39 Nkhani zina zokhudza Ahabu ndi zochita zake zonse, komanso nyumba yaminyanga ya njovu+ imene anamanga, ndi mizinda yonse imene anamanga, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.