1 Mafumu 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli. 1 Mafumu 15:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
19 Nkhani zina zokhudza Yerobowamu, momwe anamenyera nkhondo+ ndi momwe analamulirira, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
31 Nkhani zina zokhudza Nadabu ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.