Oweruza 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ehudi anafika kwa mfumuyo ili yokhayokha m’chipinda chapadera chozizira bwino, chimene chinali padenga.* Pamenepo Ehudi anati: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu.
20 Ehudi anafika kwa mfumuyo ili yokhayokha m’chipinda chapadera chozizira bwino, chimene chinali padenga.* Pamenepo Ehudi anati: “Uthenga umene ndili nawo ndi wochokera kwa Mulungu.” Atatero, mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu.