Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 23:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+

  • Ezekieli 26:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati:

      “‘“Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi! Mwa iwe munali kukhala anthu ochokera kunyanja.+ Unali wamphamvu panyanja.+ Iwe ndi anthu ako munali kuchititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.

  • Chivumbulutso 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.

  • Chivumbulutso 18:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Komanso, amalonda oyendayenda+ a padziko lapansi adzamulira+ maliro ndi kumva chisoni, chifukwa palibenso wina wowagula katundu wawo yense,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena