Yeremiya 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+ Ezekieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+ Ezekieli 27:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Adzadzimeta mpala chifukwa cha iwe+ ndi kuvala ziguduli+ ndipo adzakulirira mowawidwa mtima.+
26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+
18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+