2 Samueli 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+ Yesaya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+ Mateyu 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+
16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+
26 Zipata zake zidzalira+ ndipo zidzamva chisoni. Iye adzatsala wopanda chilichonse. Adzakhala pansi, padothi penipeni.”+
39 Choncho atapita patsogolo pang’ono, anagwada mpaka nkhope yake pansi, ndipo anapemphera+ kuti: “Atate wanga, ngati n’kotheka, kapu+ iyi indipitirire. Koma osati mwa kufuna kwanga,+ koma mwa kufuna kwanu.”+