2 Samueli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anayankha kuti: “Pamene mwana anali ndi moyo ndinali kusala kudya+ ndipo ndinali kulira+ chifukwa mumtima mwanga ndinali kunena kuti, ‘Angadziwe ndani, mwina Yehova angandikomere mtima ndipo mwanayu angakhale ndi moyo?’+ Yona 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+
22 Iye anayankha kuti: “Pamene mwana anali ndi moyo ndinali kusala kudya+ ndipo ndinali kulira+ chifukwa mumtima mwanga ndinali kunena kuti, ‘Angadziwe ndani, mwina Yehova angandikomere mtima ndipo mwanayu angakhale ndi moyo?’+
9 Ndani angadziwe? Mwina Mulungu woona satigwetsera tsoka ndipo asintha maganizo+ ndi kubweza mkwiyo wake woyaka moto, moti satiwononga.”+