2 Samueli 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+ Yoweli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+
16 Zitatero Davide anayamba kuchonderera Mulungu woona chifukwa cha mwanayo, ndipo anasiyiratu kudya.+ Kenako Davide analowa m’nyumba ndipo usiku umenewo anagona pansi.+
14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+