2 Samueli 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumu itamva zimenezi inaimirira ndi kung’amba zovala zake+ n’kugona pansi.+ Atumiki ake onse anaimirira pafupi ndi mfumuyo atang’ambanso zovala zawo.+
31 Mfumu itamva zimenezi inaimirira ndi kung’amba zovala zake+ n’kugona pansi.+ Atumiki ake onse anaimirira pafupi ndi mfumuyo atang’ambanso zovala zawo.+