Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ 2 Samueli 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri.
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri.