2 Mbiri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+ Yoweli 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa mu Ziyoni amuna inu.+ Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+
3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+
15 “Lizani lipenga la nyanga ya nkhosa mu Ziyoni amuna inu.+ Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+