Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 20:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Zitatero, ana onse a Isiraeli,+ anthu onse, anapita mpaka anakafika ku Beteli. Kumeneko analira+ ndipo anakhala pansi pamaso pa Yehova ndi kusala kudya+ tsiku limenelo mpaka madzulo. Iwo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano+ kwa Yehova.

  • Yoweli 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Konzekerani nthawi yosala kudya.+ Itanitsani msonkhano wapadera.+ Sonkhanitsani pamodzi akulu ndi anthu onse okhala m’dzikoli kuti akumane kunyumba ya Yehova Mulungu wanu+ ndipo alirire Yehova kuti awathandize.+

  • Yoweli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena