Oweruza 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu woona.+ Amuna ogwira lupanga oyenda pansi analipo 400,000.+
2 Zitatero, atsogoleri a anthu ndi mafuko onse a Isiraeli anaimirira pakati pa mpingo wonse wa anthu a Mulungu woona.+ Amuna ogwira lupanga oyenda pansi analipo 400,000.+