Levitiko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+ Levitiko 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Mukamapereka nsembe yachiyanjano kwa Yehova,+ muziipereka m’njira yakuti Mulungu akuyanjeni.+ Oweruza 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+ 1 Samueli 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”
3 “‘Ngati akupereka nsembe yachiyanjano+ kwa Yehova, ndipo akufuna kupereka ng’ombe yamphongo kapena yaikazi, azipereka yopanda chilema.+
4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
8 Choncho utsogole kupita ku Giligala.+ Inenso ndipita kumeneko kuti ndikapereke nsembe zopsereza ndi kupereka nsembe zachiyanjano.+ Ukandidikire masiku 7+ mpaka nditakupeza, ndipo ndikadzafika ndidzakuuza zoti uchite.”