Oweruza 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka mʼmawa nʼkumanga guwa lansembe ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano.+
4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka mʼmawa nʼkumanga guwa lansembe ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano.+