Oweruza 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+
4 Ndiyeno tsiku lotsatira, anthuwo anadzuka m’mawa kwambiri ndi kumanga guwa lansembe pamenepo, ndipo anapereka nsembe zopsereza+ ndi nsembe zachiyanjano.+