Ekisodo 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Mose anati: “Inuyo mutipatse nyama zokapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina, kuti tikazipereke kwa Yehova Mulungu wathu.+ Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
25 Koma Mose anati: “Inuyo mutipatse nyama zokapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zina, kuti tikazipereke kwa Yehova Mulungu wathu.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.