Yobu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anakhala+ naye limodzi pansi masiku 7 usana ndi usiku, ndipo palibe amene anali kumulankhula chilichonse popeza iwo anaona kuti ululu+ wake unali waukulu kwambiri. Yesaya 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tsika ukhale pansi pafumbi+ iwe namwali, mwana wamkazi wa Babulo.+ Khala padothi pomwe palibe mpando wachifumu,+ iwe mwana wamkazi wa Akasidi.+ Pakuti anthu adzaleka kukutchula kuti ndiwe wolekereredwa ndiponso wosasatitsidwa.*+ Maliro 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+
13 Kenako anakhala+ naye limodzi pansi masiku 7 usana ndi usiku, ndipo palibe amene anali kumulankhula chilichonse popeza iwo anaona kuti ululu+ wake unali waukulu kwambiri.
47 Tsika ukhale pansi pafumbi+ iwe namwali, mwana wamkazi wa Babulo.+ Khala padothi pomwe palibe mpando wachifumu,+ iwe mwana wamkazi wa Akasidi.+ Pakuti anthu adzaleka kukutchula kuti ndiwe wolekereredwa ndiponso wosasatitsidwa.*+
10 Akuluakulu a mwana wamkazi wa Ziyoni akhala pansi ndipo akhala chete.+Iwo athira fumbi pamitu+ yawo ndipo avala ziguduli.*+Anamwali a Yerusalemu aweramitsa mitu yawo mpaka padothi.+