Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+ Yeremiya 50:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo amadziwa kuponya mivi ndi uta komanso nthungo.+ Amenewo ndi anthu ankhanza ndipo sadzakumvera chifundo.+ Phokoso lawo lili ngati phokoso la nyanja yowinduka.+ Adzakwera pamahatchi+ ndi kukuzungulira mogwirizana n’cholinga choti akuthire nkhondo, iwe mwana wamkazi wa Babulo.+ Zekariya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Fulumira Ziyoni!+ Thawa, iwe amene ukukhala ndi mwana wamkazi wa Babulo.+
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo, amene udzafunkhidwa,+Wodala ndi amene adzakubwezera+Zimene iwe watichitira.+
42 Iwo amadziwa kuponya mivi ndi uta komanso nthungo.+ Amenewo ndi anthu ankhanza ndipo sadzakumvera chifundo.+ Phokoso lawo lili ngati phokoso la nyanja yowinduka.+ Adzakwera pamahatchi+ ndi kukuzungulira mogwirizana n’cholinga choti akuthire nkhondo, iwe mwana wamkazi wa Babulo.+