-
Yeremiya 50:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Iwo amadziwa kuponya mivi ndi uta komanso nthungo.+
Amenewo ndi anthu ankhanza ndipo sadzakumvera chifundo.+
Phokoso lawo lili ngati phokoso la nyanja imene ikuchita mafunde.+
Amachita phokosoli akakwera pamahatchi.
Mogwirizana, iwo ayalana pokonzekera kumenyana nawe, iwe mwana wamkazi wa Babulo.*+
-