Salimo 137:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+ Yesaya 13:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. 18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana.
8 Iwe mwana wamkazi wa Babulo,* amene watsala pangʼono kuwonongedwa,+Wosangalala adzakhala amene adzakubwezereZimene iwe watichitira.+
17 Ndidzachititsa Amedi kuti awaukire,+Amene saona siliva ngati kanthuNdipo sasangalala ndi golide. 18 Mauta awo adzaphwanyaphwanya anyamata.+Iwo sadzamvera chisoni chipatso cha mimbaKapena kuchitira chifundo ana.