Yesaya 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Iwo adzabangulira nyamayo m’tsiku limenelo ngati mkokomo wa nyanja.+ Munthu adzayang’ana dzikolo n’kuona kuti muli mdima womvetsa chisoni.+ Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mvula imene idzagwe m’dzikolo. Yeremiya 51:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Nyanja yasefukira ndi kumiza Babulo. Mzinda wa Babulo wamizidwa pansi pa mafunde ambiri a nyanjayo.+
30 Iwo adzabangulira nyamayo m’tsiku limenelo ngati mkokomo wa nyanja.+ Munthu adzayang’ana dzikolo n’kuona kuti muli mdima womvetsa chisoni.+ Ngakhale kuwala kudzasanduka mdima chifukwa cha mvula imene idzagwe m’dzikolo.
42 Nyanja yasefukira ndi kumiza Babulo. Mzinda wa Babulo wamizidwa pansi pa mafunde ambiri a nyanjayo.+