Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+

  • Yeremiya 4:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndinaliona dzikolo, ndipo linali lopanda kanthu ndi lachabechabe.+ Ndinayang’ana kumwamba ndipo sikunali kuwala.+

  • Yoweli 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Dziko lanjenjemera pamaso pawo ndipo kumwamba kwagwedezeka. Dzuwa ndi mwezi zada+ ndipo nyenyezi zaleka kuwala.+

  • Amosi 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limenelo ndidzachititsa kuti dzuwa lilowe masanasana,+ ndiponso kuti m’dziko mugwe mdima dzuwa lisanalowe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena