Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 15:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mkazi amene wabereka ana 7 wafooka ndipo akupuma movutikira.+ Kwa iye dzuwa lalowa masanasana,+ ndipo lachita manyazi ndi kuthedwa nzeru. Anthu otsala ndidzawapereka kwa adani awo kuti aphedwe ndi lupanga,’+ watero Yehova.”

  • Mika 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 ‘Choncho anthu inu usiku udzakufikirani,+ ndipo simudzaonanso masomphenya.+ Mudzangoona mdima wokhawokha moti simudzaloseranso. Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera ndipo mdima udzawagwera masanasana.+

  • Mateyu 24:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi+ sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba, ndipo mphamvu za kumwamba zidzagwedezeka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena