Yesaya 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Funsirani kwa lamulo ndi umboni!+ Ndithu iwo azingonena zinthu zogwirizana ndi mawu amenewa,+ koma sadzaona kuwala kwa m’bandakucha.+ Yeremiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+
20 Funsirani kwa lamulo ndi umboni!+ Ndithu iwo azingonena zinthu zogwirizana ndi mawu amenewa,+ koma sadzaona kuwala kwa m’bandakucha.+
16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+