Yesaya 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mʼmalomwake, iwo azifufuza zimene chilamulo komanso maumboni olembedwa akunena! Iwo akamalankhula zosemphana ndi mawu amenewa, ndiye kuti ali mumdima.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:20 Yesaya 1, ptsa. 121-123
20 Mʼmalomwake, iwo azifufuza zimene chilamulo komanso maumboni olembedwa akunena! Iwo akamalankhula zosemphana ndi mawu amenewa, ndiye kuti ali mumdima.*+