Yesaya 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Funsirani kwa lamulo ndi umboni!+ Ndithu iwo azingonena zinthu zogwirizana ndi mawu amenewa,+ koma sadzaona kuwala kwa m’bandakucha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:20 Yesaya 1, ptsa. 121-123
20 Funsirani kwa lamulo ndi umboni!+ Ndithu iwo azingonena zinthu zogwirizana ndi mawu amenewa,+ koma sadzaona kuwala kwa m’bandakucha.+