Yoswa 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+ Salimo 96:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,+M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+
19 Tsopano Yoswa anauza Akani kuti: “Mwana wanga, chonde, lemekeza Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ ulula kwa iye.+ Tandiuza+ chonde, n’chiyani chimene wachita? Usandibisire.”+
7 Vomerezani Yehova, inu mabanja a mitundu ya anthu,+M’patseni Yehova ulemerero ndi kuvomereza kuti iye ndi wamphamvu.+